Mkokemkoke pa za maufumu

mwnation.com · world

Pali mkokemkoke pakati pa maufumu a m’dziko lino ndi boma pa malire amene mbali ziwirizi zingatenge potsatira malamulo. Chikalata chimene adasaina mlembi wamkulu wa unduna woona za maboma aang’ono mbusa Moses Chimphepo adalemba pa 7 September. Iwo adati malamulo salola kuti m’dziko muno mukhale maufumu, kingdom m’Chingerezi, ndipo pasakhale wina wotchedwa mfumu ya mtundu. M’mbelwa … The post Mkokemkoke pa za maufumu appeared first on Nation Online .

Read full article →