A Mtsiro aiphula
Maumboni oyamikira a Ledson Mtsiro akuyenda ngati madzi m’masamba a mchezo pamene Amalawi 423 adasonkha pafupifupi K6.1 miliyoni powathokoza pa ntchito ya chitetezo imene amagwira Pa Game mu mzinda wa Lilongwe. Ndipo anthu ena a kufuna kwabwino awapatsa a Mtsiro mapuloti awiri ndipo gawo lina la ndalamazo agulira njinga ya moto komanso laputopu ya mwana … The post A Mtsiro aiphula appeared first on Nation Online .
Read full article →