Ndalama za CDF sizinafike ku makhonsolo

mwnation.com · world

Pomwe boma lakwera pa chulu kuti lapereka K85.5 biliyoni ya CDF ku makhonsolo, bungwe loona momwe makhonsolowo akuyendera makamaka pa zitukuko la Malga lati ndalamazo sizidafike ku makhonsolo. Izi zikuchitika pomwe kwatsala miyezi 6 kuti chaka cha bajeti ya 2026/27 chithe pomwe kutengera ndondomeko zatsopano zoyendetsera ndalama za CDF, ndalama zotsala zimayenera kubwerera ku boma. … The post Ndalama za CDF sizinafike ku makhonsolo appeared first on Nation Online .

Read full article →