M’nyamata wa kabaza wapsa
A motorcycle taxi driver died in a tragic accident in Lilongwe. The man, identified as Jefinala Nyambitani, was reportedly transporting fuel containers on his motorbike. Reports indicate that he and a companion were being chased by police officers. The officers wanted to stop them because of the fuel they were carrying. The death of a healthy person has caused significant pain.
Imfa iliyonse ndi yopweteka, koma yopita munthu wosadwala, ululu wake umakhala waukula kwambiri. A Jefinala Nyambitani womwe akuwaganizira kuti adanyamula zigubu za mafuta wogulitsa pa njinga yawo ya moto, amwalira imfa yomvetsa chisoni. Umu ndi m’mene zinthu zidaliri ku Lilongwe Lipoti likuti a Nyambitani ndi m’nzawo amathamangitsana ndi apolisi omwe amafuna kuwakwizinga kaamba koti adanyamula … The post M’nyamata wa kabaza wapsa appeared first on Nation Online .