A Msusa akuti mabishopu sanalandire chipondamthengo

mwnation.com · tech
Full story

Catholic Archbishop Thomas Msusa criticized bishops within his church for remaining silent regarding the problems facing Malawi. He suggested that these leaders have been accepting bribes. Msusa made these comments during a mass held at St Anthony church in Blantyre while speaking to his congregation.

Archbishop wa mpingo wa Katolika a Thomas Msusa atsutsa zoti maepikisikopi a mpingowo sakulankhula kanthu pa mavuto omwe Amalawi akukumana nawo kaamba koti adya mabanzi (adalandira ziphuphu). A Msusa adalankhula izi pa misa yomwe adachititsa pa mpingo wa St Anthony m’mzinda wa Blantyre. A Msusa kulankhula ndi atolankhani. I Nation A Archbishop amathirirapo ndemanga pa … The post A Msusa akuti mabishopu sanalandire chipondamthengo appeared first on Nation Online .

Read full article → Compare