Atuluka ku ndende pa milandu yogwiririra
Mabwalo akulu a milandu ku Zomba ndi Lilongwe apulumutsa anthu awiri omwe mabwalo a milandu a magistrate adawapeza olakwa pa milandu yogona ndi ana. Mabwalowa apereka zigamulozi nthambi ya boma yoimira anthu milandu mwaulere itawaimira posakhutitsidwa ndi zigamulo za mabwalo ocheperakowo. Iwo adagamula izi polingalira kuti a Maliko Nangwale a zaka 31 ku Zomba adali … The post Atuluka ku ndende pa milandu yogwiririra appeared first on Nation Online .