Tiyeni tigwirane manja pothana ndi mchitidwe ochitira ana nkhaza, watero Bushiri
newsare.net
Prophet Shepherd Bushiri watsindika kufunika kogwirana manja pothana ndi mchitidwe ochitira nkhaza ana ndi cholinga chokwanilitsa masomphenya a dziko lino pa chitukuko. Mneneri Bushiri wanena izi masanawa pomwe amagula katundu osiyanasiyana wa mwana wa mmudzTiyeni tigwirane manja pothana ndi mchitidwe ochitira ana nkhaza, watero Bushiri
Prophet Shepherd Bushiri watsindika kufunika kogwirana manja pothana ndi mchitidwe ochitira nkhaza ana ndi cholinga chokwanilitsa masomphenya a dziko lino pa chitukuko. Mneneri Bushiri wanena izi masanawa pomwe amagula katundu osiyanasiyana wa mwana wa mmudzi mwa mndola Mfumu yaikulu Kambwiri m’boma la Salima yemwe anadyetsedwa dowe wamuwisi ngati chilango kwa iye. Malinga ndi a Bushiri […] The post Tiyeni tigwirane manja pothana ndi mchitidwe ochitira ana nkhaza, watero Bushiri appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.