newsare.net
Mmodzi mwa anthu odziwika pa nkhani za mabizinesi akulu mdziko muno a Simbi Phiri apempha a Malawi kuti alemekeze malemu Saulos Chilima poleka kufalitsa nkhani zamabodza, miseche, kutukwanana, zipolowe komanso kuyika zithunzi zosakhala bwino pamasamba a intanSimbi apempha a Malawi: Chilima sanali waziwawa, sanali wamabodza, tiyeni timulemekeze
Mmodzi mwa anthu odziwika pa nkhani za mabizinesi akulu mdziko muno a Simbi Phiri apempha a Malawi kuti alemekeze malemu Saulos Chilima poleka kufalitsa nkhani zamabodza, miseche, kutukwanana, zipolowe komanso kuyika zithunzi zosakhala bwino pamasamba a intaneti. Poyankhula ndi atolankhani lero, a Simbi—omwe ati amawaziwa bwino a Chilima—ati a Malawi ambiri asauka nayo imfa ya […] The post Simbi apempha a Malawi: Chilima sanali waziwawa, sanali wamabodza, tiyeni timulemekeze appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more