Mabungwe oti siaboma pafupifupi 565 akhoza kuimitsidwa kugwira ntchito mdziko muno: Chachitika ndi chani?
newsare.net
Pali chiopsezo chenicheni choti mabungwe oti siaboma pafupifupi 565akhoza kuimitsidwa kugwira ntchito komanso kupatsidwa chindapusa ngati satsatira lamulo la NGO ACT. Lamuloli limaonetsetsa kuti mabungwe omwe adalembetsedwa adzipereka lipoti ku boma kudzera kMabungwe oti siaboma pafupifupi 565 akhoza kuimitsidwa kugwira ntchito mdziko muno: Chachitika ndi chani?
Pali chiopsezo chenicheni choti mabungwe oti siaboma pafupifupi 565akhoza kuimitsidwa kugwira ntchito komanso kupatsidwa chindapusa ngati satsatira lamulo la NGO ACT. Lamuloli limaonetsetsa kuti mabungwe omwe adalembetsedwa adzipereka lipoti ku boma kudzera ku bungwe loona za mmene mabungwe omwe siaboma akugwirira ntchito la Non Governmental Organizations Regulatory Authority (NGORA). Izi amayenera kuchita pofika pa […] The post Mabungwe oti siaboma pafupifupi 565 akhoza kuimitsidwa kugwira ntchito mdziko muno: Chachitika ndi chani? appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more