Mafumu apereka Ndodo ya ulemu ya Umbuya kwa a Illias Karim
newsare.net
Mafumu a ndodo a boma la Chikwawa komso Nsanje ati tsopano ndiwokhutira ndi ntchito za phungu wa kunyumba ya malamuro wa mdera la kumwera kwa boma la Chikwawa a Illias Karim. Polankhula ndi ena mwa mafumu a ndodo a maboma a Chikwawa ndi Nsanje, Mfumu yaimkulMafumu apereka Ndodo ya ulemu ya Umbuya kwa a Illias Karim
Mafumu a ndodo a boma la Chikwawa komso Nsanje ati tsopano ndiwokhutira ndi ntchito za phungu wa kunyumba ya malamuro wa mdera la kumwera kwa boma la Chikwawa a Illias Karim. Polankhula ndi ena mwa mafumu a ndodo a maboma a Chikwawa ndi Nsanje, Mfumu yaimkulu Ngowe anati a Karim ndi phungu yekhayo amene amakonda […] The post Mafumu apereka Ndodo ya ulemu ya Umbuya kwa a Illias Karim appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more