“Tipeleke Mwayi wina kwa Mai Banda kuti umoyo wa anthu usinthe” – Atero a Mwandira
newsare.net
Chipani cha Peoples(PP) chamemeza anthu kuti adzavotele mtsogoleri wawo Mai Joyce Banda yemwe adalamulira dzikoli kwa zaka ziwiri zokha kuti tsopano adzapitilize ntchito zake za chitukuko maka pa nkhani ya kupeleka mwayi kwa anthu kuchita ulimi wa ziweto ndi“Tipeleke Mwayi wina kwa Mai Banda kuti umoyo wa anthu usinthe” – Atero a Mwandira
Chipani cha Peoples(PP) chamemeza anthu kuti adzavotele mtsogoleri wawo Mai Joyce Banda yemwe adalamulira dzikoli kwa zaka ziwiri zokha kuti tsopano adzapitilize ntchito zake za chitukuko maka pa nkhani ya kupeleka mwayi kwa anthu kuchita ulimi wa ziweto ndi bizinesi za mayendedwe. Gavanala wa chipanichi Ku dera la Mbayani ,Chemusa Magasa mu mzindawu Watson Mwandira […] The post “Tipeleke Mwayi wina kwa Mai Banda kuti umoyo wa anthu usinthe” – Atero a Mwandira appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more