Amalawi ayamba kukolola zipatso za ulendo wa Chakwera ku Belgium
newsare.net
Amalawi ayamba kukolola zipatso za ulendo wa mtsogoleri wa dziko lino, Dr. Lazarus McCarthy Chakwera, ku dziko la Belgium mchaka cha 2022 pamene makampani a ku dziko la Belgium tsopano ayamba kugwira ntchito zawo mdziko muno. Imodzi mwa makampani omwe ChakwerAmalawi ayamba kukolola zipatso za ulendo wa Chakwera ku Belgium
Amalawi ayamba kukolola zipatso za ulendo wa mtsogoleri wa dziko lino, Dr. Lazarus McCarthy Chakwera, ku dziko la Belgium mchaka cha 2022 pamene makampani a ku dziko la Belgium tsopano ayamba kugwira ntchito zawo mdziko muno. Imodzi mwa makampani omwe Chakwera adakakumana nawo ku Belgium ndi Phillip Morris yomwe Lachinayi yatsimikizira Amalawi za kudzipereka kwake […] The post Amalawi ayamba kukolola zipatso za ulendo wa Chakwera ku Belgium appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more