Ras Chikomeni akugulisa chamba kusaka ndalama yopereka ku MEC kuti azayime pa chisankho 2025
newsare.net
Yemwe akufuna kudzayimira nawo pampando wa pulezidenti pa chisankho cha 2025 a Ras Chikomeni Chirwa wati wayamba kugulitsa chamba kuti apeze ndalama zomwe zimafunikira kupereka ku bungwe la MEC kuti munthu ayimire nawo pa chisankho . A Chirwa akuti mpingo wawRas Chikomeni akugulisa chamba kusaka ndalama yopereka ku MEC kuti azayime pa chisankho 2025
Yemwe akufuna kudzayimira nawo pampando wa pulezidenti pa chisankho cha 2025 a Ras Chikomeni Chirwa wati wayamba kugulitsa chamba kuti apeze ndalama zomwe zimafunikira kupereka ku bungwe la MEC kuti munthu ayimire nawo pa chisankho . A Chirwa akuti mpingo wawo wama Ras unalandira chiphaso chowavomereza kugulitsa chamba kwa chaka chimodzi kuchokera kubungwe lowona za […] The post Ras Chikomeni akugulisa chamba kusaka ndalama yopereka ku MEC kuti azayime pa chisankho 2025 appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more