Mnyamata wa zaka 17 azipha poziwombera ndi mfuti kamba kosemphana ndi chibwezi chake
newsare.net
Mnyamata wa zaka 17 Tinasha Mtawali, wadzipha ku Chitipi m’boma la Lilongwe, pa nkhani zomwe zikuganizilidwa kuti ndi za chibwenzi. Mneneri wa polisi ya Lilongwe a Hastings Chigalu wati mnyamatayu adaimbira lamya chibwenzi chake kuchiuza kuti sadzamuonaMnyamata wa zaka 17 azipha poziwombera ndi mfuti kamba kosemphana ndi chibwezi chake
Mnyamata wa zaka 17 Tinasha Mtawali, wadzipha ku Chitipi m’boma la Lilongwe, pa nkhani zomwe zikuganizilidwa kuti ndi za chibwenzi. Mneneri wa polisi ya Lilongwe a Hastings Chigalu wati mnyamatayu adaimbira lamya chibwenzi chake kuchiuza kuti sadzamuonanso. A Chigalu ati ali mkati molankhulana, bwenzi lakelo linamva kuombedwa kwa mfuti ndipo Tinasha adaleka kulankhura. Izi zidapangitsa […] The post Mnyamata wa zaka 17 azipha poziwombera ndi mfuti kamba kosemphana ndi chibwezi chake appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more