Anthu asanu ndi mmodzi amwalira, ambiri avulala pa ngozi ya ku By-pass ku Lilongwe
newsare.net
Zachitika ku msewu wa By-Pass ku Lilongwe komwe anthu asanu ndi mmodzi amwalira ndipo ena atatu avulala modetsa nkhawa pangozi ziwiri zomwe zachitikira malo amodzi. Mneneri wa polisi ya Lilongwe a Hastings Chigalu wati Lamulungu, galimoto ya mtundu wa truck yAnthu asanu ndi mmodzi amwalira, ambiri avulala pa ngozi ya ku By-pass ku Lilongwe
Zachitika ku msewu wa By-Pass ku Lilongwe komwe anthu asanu ndi mmodzi amwalira ndipo ena atatu avulala modetsa nkhawa pangozi ziwiri zomwe zachitikira malo amodzi. Mneneri wa polisi ya Lilongwe a Hastings Chigalu wati Lamulungu, galimoto ya mtundu wa truck ya kampani ya Central Poultry inali itafa, kotero inangoima pa msewu. Cha ma 7 koloko […] The post Anthu asanu ndi mmodzi amwalira, ambiri avulala pa ngozi ya ku By-pass ku Lilongwe appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more