Ena aletsedwa kuyima ku konveshoni ya MCP
newsare.net
Pali kuthekera kwakukulu kuti anthu ena omwe angolowa kumene chipani cha Malawi Congress (MCP) sakapikisana nawo ku msonkhano waukulu wachipani-chi pamene komiti yomwe ikuyendetsa msonkhanowu ikuwunikira zikalata za opikisana. Anthu omwe awonetsa chidwi kukapEna aletsedwa kuyima ku konveshoni ya MCP
Pali kuthekera kwakukulu kuti anthu ena omwe angolowa kumene chipani cha Malawi Congress (MCP) sakapikisana nawo ku msonkhano waukulu wachipani-chi pamene komiti yomwe ikuyendetsa msonkhanowu ikuwunikira zikalata za opikisana. Anthu omwe awonetsa chidwi kukapikisana nawo pa maudindo osiyana-siyana apereka zikalata zawo, koma komiti ikuwunika pofuna kupeza omwe ali ovomerezeka. Nkhalapampando wakomiti yomwe ikuyendetsa zokonzekera za […] The post Ena aletsedwa kuyima ku konveshoni ya MCP appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more