NICE ilimbikitsa mgwirizano polimbikitsa amayi, achinyamata kutengapo gawo pa masankho a mu 2025
newsare.net
Bungwe lophunzitsa ndi kuzindikiritsa anthu pa zinthu zosiyanasiyana la National Initiative for Civic Education (NIC) lamema okhudzidwa onse kuti agwirana manja pa ntchito yolimbikitsa amayi ndi achinyamata kutengapo gawo pa masankho a mchaka chamawa. Mkulu wNICE ilimbikitsa mgwirizano polimbikitsa amayi, achinyamata kutengapo gawo pa masankho a mu 2025
Bungwe lophunzitsa ndi kuzindikiritsa anthu pa zinthu zosiyanasiyana la National Initiative for Civic Education (NIC) lamema okhudzidwa onse kuti agwirana manja pa ntchito yolimbikitsa amayi ndi achinyamata kutengapo gawo pa masankho a mchaka chamawa. Mkulu wa bungweli a Gray Kalindekafe ndi amene adapereka pempholi m’boma la Dedza masiku apitawa pamene amakhazikitsidwa ngati Katswiri Wachimuna (Male Champion) wa […] The post NICE ilimbikitsa mgwirizano polimbikitsa amayi, achinyamata kutengapo gawo pa masankho a mu 2025 appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more