Loya Bright Theu wadabwa kuti a Chakwera ndi mkulu wa Polisi sakuyankhulapo za zipolowe
newsare.net
Mmodzi mwa a katswiri pa nkhani za malamulo mdziko muno a Bright Theu adzudzula mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ndi mkulu wa apolosi mayi Merlyne Yolam ati pokhala chete pamene gulu la zigawenga lakhala likusokoneza ziwonetsero mzinda wa LilongweLoya Bright Theu wadabwa kuti a Chakwera ndi mkulu wa Polisi sakuyankhulapo za zipolowe
Mmodzi mwa a katswiri pa nkhani za malamulo mdziko muno a Bright Theu adzudzula mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ndi mkulu wa apolosi mayi Merlyne Yolam ati pokhala chete pamene gulu la zigawenga lakhala likusokoneza ziwonetsero mzinda wa Lilongwe pogwiritsa ntchito zikwanje, mipeni ndi zida zina. Polemba pa tsamba lawo la mchezo […] The post Loya Bright Theu wadabwa kuti a Chakwera ndi mkulu wa Polisi sakuyankhulapo za zipolowe appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more