Tobias akumbutsa aMalawi za kufunikira kovotera mtsogoleri wangwiro komanso wa masomphenya
newsare.net
Yemwe akufuna kudzayimira nawo pa mpikisano wa mtsogoleri wa dziko, a Milward Tobias, alangiza aMalawi za kufunikira kosankha mtsogoleri wa masomphenya komanso luntha ndi chidziwitso pa mmene chuma cha dziko chikuyendera. Ndipo a Tobias – yemwe ndi mkadaulTobias akumbutsa aMalawi za kufunikira kovotera mtsogoleri wangwiro komanso wa masomphenya
Yemwe akufuna kudzayimira nawo pa mpikisano wa mtsogoleri wa dziko, a Milward Tobias, alangiza aMalawi za kufunikira kosankha mtsogoleri wa masomphenya komanso luntha ndi chidziwitso pa mmene chuma cha dziko chikuyendera. Ndipo a Tobias – yemwe ndi mkadaulo pa nkhani za chuma – ati iwowo ndi munthu yekhayo yemwe pakali pano wadzipereka kudzatumikira dziko lino […] The post Tobias akumbutsa aMalawi za kufunikira kovotera mtsogoleri wangwiro komanso wa masomphenya appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more