Chakwera wayamba kugawa chakudya kwa a Malawi osowa: Mabanja 1200 athandizidwa ku Mulanje
newsare.net
Ntchito yogawa chimanga ku mabanja omwe akhudzidwa ndi njala m’boma la Mulanje yayamba lero, lolemba kwa Mthiramanja komwe mabanja 1200 alandira chimangachi. DC wa boma la Mulanje a David Kayiwonanga Gondwe ati mabanja 69,497 ndiwo alandire chimanga mChakwera wayamba kugawa chakudya kwa a Malawi osowa: Mabanja 1200 athandizidwa ku Mulanje
Ntchito yogawa chimanga ku mabanja omwe akhudzidwa ndi njala m’boma la Mulanje yayamba lero, lolemba kwa Mthiramanja komwe mabanja 1200 alandira chimangachi. DC wa boma la Mulanje a David Kayiwonanga Gondwe ati mabanja 69,497 ndiwo alandire chimanga m’boma lonse la Mulanje kwa miyezi isanu m’bomali. A Gondwe apempha anthu kuti apewe chisokonezo ndi ziwawa pa […] The post Chakwera wayamba kugawa chakudya kwa a Malawi osowa: Mabanja 1200 athandizidwa ku Mulanje appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more