Boma la German lapereka ndalama zokwana K35 billion kudziko la Malawi za mtukula pakhomo
newsare.net
Boma la Dziko la German lero lapereka ndama zokwana K35 billion zomwe zigwire ntchito ya mtukula pakhomo. Mukulankhula kwawo, nduna yazachuma a Simplex Chithyola Banda adayamika boma la Germany kamba ka thandizo la chuma chochuluka onga ichi. A Chithyola alonBoma la German lapereka ndalama zokwana K35 billion kudziko la Malawi za mtukula pakhomo
Boma la Dziko la German lero lapereka ndama zokwana K35 billion zomwe zigwire ntchito ya mtukula pakhomo. Mukulankhula kwawo, nduna yazachuma a Simplex Chithyola Banda adayamika boma la Germany kamba ka thandizo la chuma chochuluka onga ichi. A Chithyola alonjeza dziko la German kuti ligwiritsa ncthito bwino chuma chomwe boma la German lapereka ku boma […] The post Boma la German lapereka ndalama zokwana K35 billion kudziko la Malawi za mtukula pakhomo appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more