Chakwera akhululukira akaidi 35
newsare.net
Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera akhululukira akaidi 35 ngati mbali imodzi ya chisangalalo choti dziko lino lakwanisa zaka 60 zodzilamulira kuchoka m’manja mwa atsamunda. Malingana ndi kalata yomwe watulutsa unduna wa za m’dziko ndipo wChakwera akhululukira akaidi 35
Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera akhululukira akaidi 35 ngati mbali imodzi ya chisangalalo choti dziko lino lakwanisa zaka 60 zodzilamulira kuchoka m’manja mwa atsamunda. Malingana ndi kalata yomwe watulutsa unduna wa za m’dziko ndipo wasainira ndi mlembi wamkulu a Steve Kayuni, a Chakwera agwiritsa ntchito mphamvu zomwe malamulo aakulu a dziko lino amamupatsa […] The post Chakwera akhululukira akaidi 35 appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more