Bungwe la Red Cross Malawi lapeleka Maphunziro apadera kwa atolankhani mu mzinda wa Blantyre
newsare.net
Bungwe la Red Cross Malawi lomwe limaona ndi kuyendetsa za chitetezo ,ufulu ndi thandizo la anthu launikira atolankha pa zomwe anthu amayenera kutsata mu nthawi ya zipwilikiti za nkhondo kuti iwo pamodzi ndi anthuwa molingana ndi lamulo la m’maiko omweBungwe la Red Cross Malawi lapeleka Maphunziro apadera kwa atolankhani mu mzinda wa Blantyre
Bungwe la Red Cross Malawi lomwe limaona ndi kuyendetsa za chitetezo ,ufulu ndi thandizo la anthu launikira atolankha pa zomwe anthu amayenera kutsata mu nthawi ya zipwilikiti za nkhondo kuti iwo pamodzi ndi anthuwa molingana ndi lamulo la m’maiko omwe bungweli likugwiramo ntchito lotchedwa International Humanitarian Law(IHL) m’malamulo ankhondo ,ufulu komanso chitetezo cha anthu kuti […] The post Bungwe la Red Cross Malawi lapeleka Maphunziro apadera kwa atolankhani mu mzinda wa Blantyre appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.