Kukoma Ntopwa yalandira thandizo la K10 miliyoni
newsare.net
Kampani ya Capital Oil Refining Industries (Cori) yathandiza timu yampira wamiyendo koma osewera ake ali akazi ya Kukoma Ntopwa ndi ndalama zokwana 10 miliyoni Kwacha kuti zithandizire timuyi pamene ikukachita nawo mpikisano wa chaka chino wa COSAFA womwensoKukoma Ntopwa yalandira thandizo la K10 miliyoni
Kampani ya Capital Oil Refining Industries (Cori) yathandiza timu yampira wamiyendo koma osewera ake ali akazi ya Kukoma Ntopwa ndi ndalama zokwana 10 miliyoni Kwacha kuti zithandizire timuyi pamene ikukachita nawo mpikisano wa chaka chino wa COSAFA womwenso ukathandizire kupeza matimu oti alowe nawo mu mpikisano wa CAF Women’s Champions League. Timuyi inyamuka kupita […] The post Kukoma Ntopwa yalandira thandizo la K10 miliyoni appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more