A Joyce Banda, a Muluzi, a APM auza mkulu wa polisi kuti amange anthu omwe anayambisa zipolowe ku Lilongwe
newsare.net
Omwe adakhalapo atsogoleri a dziko lino auza mkulu wa polisi a Merlyene Yolamu kuti afufuze komanso kumanga anthu omwe adachitira anthu nkhaza ndikuletsa zionetsero za zipani zotsutsa boma Lachitatu munzinda wa Lilongwe. Atsogoleriwa, a Bakili Muluzi,A Joyce Banda, a Muluzi, a APM auza mkulu wa polisi kuti amange anthu omwe anayambisa zipolowe ku Lilongwe
Omwe adakhalapo atsogoleri a dziko lino auza mkulu wa polisi a Merlyene Yolamu kuti afufuze komanso kumanga anthu omwe adachitira anthu nkhaza ndikuletsa zionetsero za zipani zotsutsa boma Lachitatu munzinda wa Lilongwe. Atsogoleriwa, a Bakili Muluzi, a Joyce Banda komanso a Peter Mutharika, ati Amalawi akuyenera kupatsidwa mpata ochita zionetsero komanso kusankha atsogoleri akumtima […] The post A Joyce Banda, a Muluzi, a APM auza mkulu wa polisi kuti amange anthu omwe anayambisa zipolowe ku Lilongwe appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more