UTM ipikisana nawo mchisankho cha chaka chamawa, watero Patricia Kaliati
newsare.net
A Kaliati ati UTM idakali ya mphamvu mzigawo zonse za mdziko lino ngakhale mtsogoleri wawo a Saulos Chilima adamwalira pa ngozi ya ndege. Iwo ati akamaliza kukhuza maliro a Chilima ndi anthu ena asanu ndi atatu chipanichi chichititsa misokhano mzigawo zonse kUTM ipikisana nawo mchisankho cha chaka chamawa, watero Patricia Kaliati
A Kaliati ati UTM idakali ya mphamvu mzigawo zonse za mdziko lino ngakhale mtsogoleri wawo a Saulos Chilima adamwalira pa ngozi ya ndege. Iwo ati akamaliza kukhuza maliro a Chilima ndi anthu ena asanu ndi atatu chipanichi chichititsa misokhano mzigawo zonse kuwuza Amalawi za tsogolo la chipanichi. “Mchipani chathu mukulowa anthu a zipani zosiyanasiyana kufuna […] The post UTM ipikisana nawo mchisankho cha chaka chamawa, watero Patricia Kaliati appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more