Chaponda akuti a Chakwera atulutse lipoti la Ngozi ya ndege ku Chikangawa
newsare.net
A George Chaponda, omwe ndi mtsogoleri otsutsa boma ku nyumba ya malamulo, wauza President Lazarus Chakwera kuti atulutse nsanga zotsatira za kafukufuku wa ngozi ya ndege yomwe idapha a Saulos Chilima ndi anthu ena asanu ndi atatu pa 10 June chaka chino. A ChChaponda akuti a Chakwera atulutse lipoti la Ngozi ya ndege ku Chikangawa
A George Chaponda, omwe ndi mtsogoleri otsutsa boma ku nyumba ya malamulo, wauza President Lazarus Chakwera kuti atulutse nsanga zotsatira za kafukufuku wa ngozi ya ndege yomwe idapha a Saulos Chilima ndi anthu ena asanu ndi atatu pa 10 June chaka chino. A Chaponda ati a Chakwera adauza mtolankhani wa DW kuti akatswiri aku Germany […] The post Chaponda akuti a Chakwera atulutse lipoti la Ngozi ya ndege ku Chikangawa appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more