Khonsolo ya Lilongwe yayamba kugwesa ma shop omangidwa malo osalolezedwa m’muzindawu
newsare.net
Khonsolo ya mzinda wa Lilongwe m’bandakucha wa lero yagwetsa nyumba zomwe anthu ena anamanga ku Malangalanga mu mzinda wa Lilongwe. Malingana ndi mneneri wa khonsoloyi a Tamara Chafunya, nyumba zina zomwe eni ake anatenga chiletso ku khothi kuti asawagwKhonsolo ya Lilongwe yayamba kugwesa ma shop omangidwa malo osalolezedwa m’muzindawu
Khonsolo ya mzinda wa Lilongwe m’bandakucha wa lero yagwetsa nyumba zomwe anthu ena anamanga ku Malangalanga mu mzinda wa Lilongwe. Malingana ndi mneneri wa khonsoloyi a Tamara Chafunya, nyumba zina zomwe eni ake anatenga chiletso ku khothi kuti asawagwetsere, azisiya kaye pakadali pano. Iwo ati ntchitoyi akhala akuyigwira m’malo ochitira malonda komanso okhala anthu, ngakhale […] The post Khonsolo ya Lilongwe yayamba kugwesa ma shop omangidwa malo osalolezedwa m’muzindawu appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more