newsare.net
Patangodusa mwezi umodzi pomwe bamboo wina anawombera mkazi mpaka imfa ku Dedza, thambo lakuda lagwanso mubomali pomwe mayi wina m’mudzi mwa Yahaya pa boma ku Dedza wafa atamenyedwa ndi mamuna wake. Mfumu Yahaya yauza Nyasatimes kuti mayiyu ndi mamuna wZachitikanso ku Dedza: Bambo amenya mkazi wake mpaka kufa
Patangodusa mwezi umodzi pomwe bamboo wina anawombera mkazi mpaka imfa ku Dedza, thambo lakuda lagwanso mubomali pomwe mayi wina m’mudzi mwa Yahaya pa boma ku Dedza wafa atamenyedwa ndi mamuna wake. Mfumu Yahaya yauza Nyasatimes kuti mayiyu ndi mamuna wake onse anali ku mowa dzulo koma anayamba kukangana kumeneko kamba koti mkazi wake amalankhula ndi […] The post Zachitikanso ku Dedza: Bambo amenya mkazi wake mpaka kufa appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more