newsare.net
Nduna ya zofalitsa nkhani yemwenso ndi m’neneri wa boma a Moses Kunkuyu wati kutsegula ofesi ya ukazembe m’dziko la Israel kuthandiza kuthana ndi mavuto omwe achinyamata akhathe kukumana nawo pomwe akugwila ntchito m’dzikoli. A Kunkuyu ayakhBoma latsimikiza za chitetezo chokhazikika kwa achinyamata omwe akugwila ntchito dziko la Israel
Nduna ya zofalitsa nkhani yemwenso ndi m’neneri wa boma a Moses Kunkuyu wati kutsegula ofesi ya ukazembe m’dziko la Israel kuthandiza kuthana ndi mavuto omwe achinyamata akhathe kukumana nawo pomwe akugwila ntchito m’dzikoli. A Kunkuyu ayakhula izi pa msokhano wa olemba nkhani ku Lilongwe pomwe mwa zina amatambasula za ulendo wawo wa ku Israel pamodzi […] The post Boma latsimikiza za chitetezo chokhazikika kwa achinyamata omwe akugwila ntchito dziko la Israel appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more