newsare.net
Mtsogoleri wa dziko lino Dr. Lazarus McCarthy Chakwera wapempha aMalawi kuti asalolere kuti mdyerekezi agwiritse ntchito imfa zowawa zomwe dziko lino lakumana nazo pakatipa pobweretsa kugawanikana pakati pa anthu. Chakwera wapemphanso mkulu wa apolisi mdzikoTisalole kuti imfa zowawa takumana nazozi zisatigawanitse ngati dziko – Chakwera
Mtsogoleri wa dziko lino Dr. Lazarus McCarthy Chakwera wapempha aMalawi kuti asalolere kuti mdyerekezi agwiritse ntchito imfa zowawa zomwe dziko lino lakumana nazo pakatipa pobweretsa kugawanikana pakati pa anthu. Chakwera wapemphanso mkulu wa apolisi mdziko muno kuti awonetsetese kuti nthambi ya polisi ikutumiradi anthu osati kuzunza anthu. Iye wanene izi mu mzinda wa Lilongwe pamwambo […] The post Tisalole kuti imfa zowawa takumana nazozi zisatigawanitse ngati dziko – Chakwera appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more