newsare.net
Wachiwiri kwa mtsogoleri wachipani cha DPP mchigawo chaku mmawa a Bright Msaka wati ndiokondwa kuti chipanichi chatenga mipando yonse ya m’makhonsolo mchigawochi. A Msaka ayankhula izi pambuyo pa chisankho cha wapampando wa khonsolo ya boma la MachingaDPP yasosola mipando yambiri ya mankhasala ku Eastern Region
Wachiwiri kwa mtsogoleri wachipani cha DPP mchigawo chaku mmawa a Bright Msaka wati ndiokondwa kuti chipanichi chatenga mipando yonse ya m’makhonsolo mchigawochi. A Msaka ayankhula izi pambuyo pa chisankho cha wapampando wa khonsolo ya boma la Machinga. Khansala Simplex Diwa wasankhidwa kukhala wapampando ndipo wachiwiri wake ndi khansala Davis Weja. A Diwa ati […] The post DPP yasosola mipando yambiri ya mankhasala ku Eastern Region appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more