newsare.net
Mtsogoleri wa zipani zotsutsa boma m’nyumba ya malamulo, a George Chaponda, wati ali okonzeka kupereka umboni woti bungwe la National Registration Bureau (NRB) likusindikiza ziphaso za umunthu zatsopano ku Kanengo, Lilongwe. Izi zatsatira pempho lachitidwaA Chaponda akuti ali okonzeka kupereka umboni pa nkhani yoti NRB ikusindikiza ma ID ku Kanengo
Mtsogoleri wa zipani zotsutsa boma m’nyumba ya malamulo, a George Chaponda, wati ali okonzeka kupereka umboni woti bungwe la National Registration Bureau (NRB) likusindikiza ziphaso za umunthu zatsopano ku Kanengo, Lilongwe. Izi zatsatira pempho lachitidwa lero m’nyumba ya malamulo ndi phungu wa dera la Chitipa South, a Werani Chilenga, omwe anapempha kuti a Chaponda apereke […] The post A Chaponda akuti ali okonzeka kupereka umboni pa nkhani yoti NRB ikusindikiza ma ID ku Kanengo appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more