newsare.net
Yemwe akufuna kudzayimira nawo pa udindo wa mtsogoleri wa dziko, Milward Tobias, wati kuthetsa ndalenza zipani ndi njira imodzi yomwe ingathandize potukula dziko lino. Tobias wati ndi chifukwa chake iye akufuna kudzayimira nawo pa mpandowu posayimira chipaniKuchotsa ndale za zipani kungathandize kusintha dziko lino – Tobias
Yemwe akufuna kudzayimira nawo pa udindo wa mtsogoleri wa dziko, Milward Tobias, wati kuthetsa ndalenza zipani ndi njira imodzi yomwe ingathandize potukula dziko lino. Tobias wati ndi chifukwa chake iye akufuna kudzayimira nawo pa mpandowu posayimira chipani chilichonse. “Ine Milward Tobias ndidzaima pa udindo wa mtsogoleri wa dziko chisankho cha pa 16 September chaka chino. […] The post Kuchotsa ndale za zipani kungathandize kusintha dziko lino – Tobias appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more