newsare.net
Bungwe lopeleka ngongole la NEEF lati ndilokhudzika ndi kuchepa kwa chiwelengero cha achinyamata omwe akuonetsa chidwi chotenga nawo ngongole zake m’dziko muno. Mkulu wa bungwe a Humphrey Mdyetseni anena izi pa mkumano wolimbikitsa ndi kudziwitsa achinyAchinyamata sakuonetsa chidwi chopeza nawo ngongole ya NEEF–Watero mkulu wa NEEF a Mdyetseni
Bungwe lopeleka ngongole la NEEF lati ndilokhudzika ndi kuchepa kwa chiwelengero cha achinyamata omwe akuonetsa chidwi chotenga nawo ngongole zake m’dziko muno. Mkulu wa bungwe a Humphrey Mdyetseni anena izi pa mkumano wolimbikitsa ndi kudziwitsa achinyamata za ubwino wotenga ngongole ya NEEF la Chiwiri mu mzinda wa Blantyre. Amdyetse ati mwa ngongole za ndalama zokwana […] The post Achinyamata sakuonetsa chidwi chopeza nawo ngongole ya NEEF–Watero mkulu wa NEEF a Mdyetseni appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more