newsare.net
Mtsogoleli wa chipani cha UTM a Dalitso Kabambe ati anthu akawasakha pa udindo wa mtsogoleli wa dziko lino pa zisakho za pa 16 September adzayetsetsa kutsitsa ndalama ya msonkho yomwe anthu ogwila ntchito amapeleka ku boma malinga ndi momwe amalandila, Pay AKabambe walonjeza kudzatsitsa Msonkho Wapamalipiro a Anthu Ogwira Ntchito [PAYE]
Mtsogoleli wa chipani cha UTM a Dalitso Kabambe ati anthu akawasakha pa udindo wa mtsogoleli wa dziko lino pa zisakho za pa 16 September adzayetsetsa kutsitsa ndalama ya msonkho yomwe anthu ogwila ntchito amapeleka ku boma malinga ndi momwe amalandila, Pay As You Earn (PAYE) pa chizungu. Iwo ati anthu m’dziko muno kuphatikizapo ogwila ntchito […] The post Kabambe walonjeza kudzatsitsa Msonkho Wapamalipiro a Anthu Ogwira Ntchito [PAYE] appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more