newsare.net
Bungwe lomenyera ufulu wa anthu la Human Rights Defenders Coalition (HRDC) lati layika chidwi chake pokambirana ndi adindo za mavuto omwe ali mdziko muno ndikupeza mayankho osati kuchita zionetsero. Izi zadza pamene magulu ena okhudzidwa akonza zionetsero mziBungwe la HRDC likuti iwowo ziwonetsero ayi, iwo asankha njira yokambirana ndi adindo
Bungwe lomenyera ufulu wa anthu la Human Rights Defenders Coalition (HRDC) lati layika chidwi chake pokambirana ndi adindo za mavuto omwe ali mdziko muno ndikupeza mayankho osati kuchita zionetsero. Izi zadza pamene magulu ena okhudzidwa akonza zionetsero mzigawo zonse za dziko lino pa 10 mwezi uno kusonyeza kukwiya ndi momwe zinthu zikuyendera mdziko muno. Mkulu […] The post Bungwe la HRDC likuti iwowo ziwonetsero ayi, iwo asankha njira yokambirana ndi adindo appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more