newsare.net
Bungwe lomenyera Ufulu wa anthu omwe ali ndi ulumali wosiyanasiyana la CHRR mongwirizana ndi bungwe loyang’anira mabungwe ena pa nkhaniyi, la MACODA likuchititsa mkumano wounikira anthuwa pa ufulu omwe amawalora kulumikizitsidwa bwino lomwe pa nkhani yMabungwe à CHRR ndi MACODA a kulimbikitsa anthu aulumali kudziwa Ufulu wawo bwino,kutsatira zisankho
Bungwe lomenyera Ufulu wa anthu omwe ali ndi ulumali wosiyanasiyana la CHRR mongwirizana ndi bungwe loyang’anira mabungwe ena pa nkhaniyi, la MACODA likuchititsa mkumano wounikira anthuwa pa ufulu omwe amawalora kulumikizitsidwa bwino lomwe pa nkhani ya zisankho ndi muzipani za ndale m’dziko muno. Mkumanowu womwe ndi wamasiku awiri ukuchitikira mu mzinda wa Blantyre wayamba lachisanu […] The post Mabungwe à CHRR ndi MACODA a kulimbikitsa anthu aulumali kudziwa Ufulu wawo bwino,kutsatira zisankho appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more